4 “Iye adzaimirira n’kuyamba kuweta nkhosa mu mphamvu ya Yehova+ ndiponso m’dzina lalikulu la Yehova Mulungu wake.+ Anthuwo azidzakhala kumeneko motetezeka,+ pakuti iye adzakhala wamkulu mpaka kumalekezero a dziko lapansi.+
55 Mu ola lomwelo Yesu anafunsa khamu la anthulo kuti: “Bwanji mwabwera kudzandigwira mutatenga malupanga ndi zibonga ngati mukukalimbana ndi wachifwamba?+ Tsiku ndi tsiku ndinali kukhala pansi m’kachisi+ ndi kuphunzitsa, koma simunandigwire.