1 Samueli 17:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Pamenepo ine ndinatsatira chilombocho n’kuchipha,+ ndipo ndinapulumutsa nkhosa m’kamwa mwake. Chitayamba kundiukira, ndinagwira ndevu zake, n’kuchikantha ndi kuchipha. Yesaya 53:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye anapanikizidwa+ ndipo analola kuti asautsidwe,+ koma sanatsegule pakamwa pake. Anatengedwa ngati nkhosa yopita kokaphedwa,+ ndipo mofanana ndi nkhosa yaikazi imene imakhala chete akamaimeta ubweya, nayenso sanatsegule pakamwa pake.+ Aheberi 13:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsopano, Mulungu wamtendere,+ amene anaukitsa kwa akufa+ m’busa wamkulu+ wa nkhosa+ wokhala ndi magazi a pangano losatha,+ Ambuye wathu Yesu,
35 Pamenepo ine ndinatsatira chilombocho n’kuchipha,+ ndipo ndinapulumutsa nkhosa m’kamwa mwake. Chitayamba kundiukira, ndinagwira ndevu zake, n’kuchikantha ndi kuchipha.
7 Iye anapanikizidwa+ ndipo analola kuti asautsidwe,+ koma sanatsegule pakamwa pake. Anatengedwa ngati nkhosa yopita kokaphedwa,+ ndipo mofanana ndi nkhosa yaikazi imene imakhala chete akamaimeta ubweya, nayenso sanatsegule pakamwa pake.+
20 Tsopano, Mulungu wamtendere,+ amene anaukitsa kwa akufa+ m’busa wamkulu+ wa nkhosa+ wokhala ndi magazi a pangano losatha,+ Ambuye wathu Yesu,