Mateyu 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mwachitsanzo, maganizo oipa, za kupha anthu, za chigololo, za dama, za kuba, maumboni onama, ndi zonyoza Mulungu,+ zimachokera mumtima.+ Luka 22:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma Satana analowa mwa Yudasi, wotchedwa Isikariyoti, mmodzi wa ophunzira 12 aja.+ Yohane 13:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Atamupatsa chidutswa cha mkatecho, pamenepo Satana analowa mwa Yudasi.+ Chotero Yesu anamuuza kuti: “Zimene wakonza kuchita, zichite mwamsanga.” Machitidwe 1:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 kuti atenge malo a utumiki uwu ndi utumwi,+ amene Yudasi anawasiya ndi kuyenda njira zake.”
19 Mwachitsanzo, maganizo oipa, za kupha anthu, za chigololo, za dama, za kuba, maumboni onama, ndi zonyoza Mulungu,+ zimachokera mumtima.+
27 Atamupatsa chidutswa cha mkatecho, pamenepo Satana analowa mwa Yudasi.+ Chotero Yesu anamuuza kuti: “Zimene wakonza kuchita, zichite mwamsanga.”