Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 26:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Pambuyo pake mmodzi wa ophunzira 12 aja, wotchedwa Yudasi Isikariyoti,+ anapita kwa ansembe aakulu

  • Maliko 14:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Kenako Yudasi Isikariyoti, mmodzi wa ophunzira 12 aja, anachoka ndi kupita kwa ansembe aakulu kuti akapereke Yesu kwa iwo.+

  • Yohane 6:70
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 70 Pamenepo Yesu anati: “Ine ndinakusankhani inu 12,+ si choncho kodi? Komatu mmodzi wa inu ndi wonenera anzake zoipa.”+

  • Yohane 13:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Chakudya chamadzulo chili mkati, Mdyerekezi anali ataika kale maganizo ofuna kupereka Yesu+ mumtima mwa Yudasi Isikariyoti,+ mwana wa Simoni.

  • Yohane 13:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Atamupatsa chidutswa cha mkatecho, pamenepo Satana analowa mwa Yudasi.+ Chotero Yesu anamuuza kuti: “Zimene wakonza kuchita, zichite mwamsanga.”

  • Machitidwe 1:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 chifukwa anali mmodzi wa ife,+ ndipo anali kutumikira nafe limodzi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena