Luka 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Komanso anasankha Yudasi mwana wa Yakobo, ndi Yudasi Isikariyoti, amene pambuyo pake anam’pereka.+ Yohane 6:71 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 71 Kwenikweni iye anali kunena za Yudasi mwana wa Simoni Isikariyoti, pakuti ameneyu anali kudzamupereka,+ ngakhale anali mmodzi wa ophunzira 12 amenewo.
16 Komanso anasankha Yudasi mwana wa Yakobo, ndi Yudasi Isikariyoti, amene pambuyo pake anam’pereka.+
71 Kwenikweni iye anali kunena za Yudasi mwana wa Simoni Isikariyoti, pakuti ameneyu anali kudzamupereka,+ ngakhale anali mmodzi wa ophunzira 12 amenewo.