Maliko 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 ndi Yudasi Isikariyoti, amene pambuyo pake anadzam’pereka.+ Kenako Yesu analowa m’nyumba.