Mateyu 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Simoni Kananiya,*+ ndi Yudasi Isikariyoti, amene pambuyo pake anapereka+ Yesu. Luka 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Komanso anasankha Yudasi mwana wa Yakobo, ndi Yudasi Isikariyoti, amene pambuyo pake anam’pereka.+
16 Komanso anasankha Yudasi mwana wa Yakobo, ndi Yudasi Isikariyoti, amene pambuyo pake anam’pereka.+