Salimo 109:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Muikireni woweruza woipa,Ndipo kudzanja lake lamanja kuime wotsutsana naye.+ Luka 22:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma Satana analowa mwa Yudasi, wotchedwa Isikariyoti, mmodzi wa ophunzira 12 aja.+