Mateyu 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Simoni Kananiya,*+ ndi Yudasi Isikariyoti, amene pambuyo pake anapereka+ Yesu. Luka 22:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma Satana analowa mwa Yudasi, wotchedwa Isikariyoti, mmodzi wa ophunzira 12 aja.+ Yohane 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chakudya chamadzulo chili mkati, Mdyerekezi anali ataika kale maganizo ofuna kupereka Yesu+ mumtima mwa Yudasi Isikariyoti,+ mwana wa Simoni.
2 Chakudya chamadzulo chili mkati, Mdyerekezi anali ataika kale maganizo ofuna kupereka Yesu+ mumtima mwa Yudasi Isikariyoti,+ mwana wa Simoni.