1 Atesalonika 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiye chifukwa chake pamene sindinathenso kupirira, ndinamutuma kuti ndidziwe za kukhulupirika+ kwanu, kuti mwina mwa njira ina, Woyesayo+ angakhale atakuyesani, ndipo ntchito imene tinagwira mwakhama ingakhale itapita pachabe.+
5 Ndiye chifukwa chake pamene sindinathenso kupirira, ndinamutuma kuti ndidziwe za kukhulupirika+ kwanu, kuti mwina mwa njira ina, Woyesayo+ angakhale atakuyesani, ndipo ntchito imene tinagwira mwakhama ingakhale itapita pachabe.+