Chivumbulutso 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chizindikiro chinanso chinaoneka kumwamba, ndipo ndinaona chinjoka chachikulu+ chofiira, chokhala ndi mitu 7 ndi nyanga 10, ndipo pamitupo panali zisoti zachifumu 7. Chivumbulutso 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako anagwira chinjoka,+ njoka yakale ija,+ amene ndi Mdyerekezi+ ndiponso Satana,+ ndi kumumanga zaka 1,000.
3 Chizindikiro chinanso chinaoneka kumwamba, ndipo ndinaona chinjoka chachikulu+ chofiira, chokhala ndi mitu 7 ndi nyanga 10, ndipo pamitupo panali zisoti zachifumu 7.
2 Kenako anagwira chinjoka,+ njoka yakale ija,+ amene ndi Mdyerekezi+ ndiponso Satana,+ ndi kumumanga zaka 1,000.