Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 6:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndiyeno ana a Mulungu+ woona anayamba kuona+ kuti ana aakazi a anthu anali okongola. Chotero, anayamba kudzitengera okha akazi alionse amene anawasankha.

  • Deuteronomo 33:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndipo anati:

      “Yehova anafika kuchokera ku Sinai,+

      Anathwanima pa iwo kuchokera ku Seiri.+

      Anawala kuchokera kudera lamapiri la Parana,+

      Ndipo anali ndi miyandamiyanda ya oyera ake,+

      Kudzanja lake lamanja kunali ankhondo ake.+

  • Yobu 38:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Pamene nyenyezi za m’mawa+ zinafuula pamodzi mokondwera,

      Ndiponso pamene ana onse a Mulungu+ anayamba kufuula ndi chisangalalo?

  • Danieli 3:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ndiyeno mfumu inati: “Taonani! Inetu ndikuona amuna amphamvu anayi akuyendayenda pakati pa moto osapsa, ndipo munthu wachinayiyo akuoneka ngati mulungu.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena