Yobu 38:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamene nyenyezi za m’mawa+ zinafuula pamodzi mokondwera,Ndiponso pamene ana onse a Mulungu+ anayamba kufuula ndi chisangalalo? Salimo 34:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mngelo wa Yehova amamanga msasa mozungulira onse oopa Mulungu,+Ndipo amawapulumutsa.+
7 Pamene nyenyezi za m’mawa+ zinafuula pamodzi mokondwera,Ndiponso pamene ana onse a Mulungu+ anayamba kufuula ndi chisangalalo?