1 Mbiri 16:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Vomerezani Yehova, inu mabanja a mitundu ya anthu,M’patseni Yehova ulemerero ndi kuvomereza kuti iye ndi wamphamvu.+ Salimo 96:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Vomerezani Yehova, inu mabanja a mitundu ya anthu,+M’patseni Yehova ulemerero ndi kuvomereza kuti iye ndi wamphamvu.+ Habakuku 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mulungu anabwera kuchokera ku Temani, Woyerayo anabwera kuchokera kuphiri la Parana.+ [Seʹlah.]+ Ulemerero wake unaphimba kumwamba+ ndipo dziko lonse linamutamanda.+
28 Vomerezani Yehova, inu mabanja a mitundu ya anthu,M’patseni Yehova ulemerero ndi kuvomereza kuti iye ndi wamphamvu.+
7 Vomerezani Yehova, inu mabanja a mitundu ya anthu,+M’patseni Yehova ulemerero ndi kuvomereza kuti iye ndi wamphamvu.+
3 Mulungu anabwera kuchokera ku Temani, Woyerayo anabwera kuchokera kuphiri la Parana.+ [Seʹlah.]+ Ulemerero wake unaphimba kumwamba+ ndipo dziko lonse linamutamanda.+