Salimo 63:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho ndakuonani m’malo oyera,+Chifukwa ndaona mphamvu zanu ndi ulemerero wanu.+ Salimo 68:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Vomerezani kuti Mulungu ndi wamphamvu zochuluka.+Iye akulamulira Isiraeli ndipo mphamvu zake zili m’mitambo.+ Salimo 115:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 115 Ife sitikuyenerera kalikonse, inu Yehova, ife sitikuyenerera kalikonse,+Koma dzina lanu ndi loyenera kulemekezedwa+Malinga ndi kukoma mtima kwanu kosatha, malinganso ndi choonadi chanu.+
34 Vomerezani kuti Mulungu ndi wamphamvu zochuluka.+Iye akulamulira Isiraeli ndipo mphamvu zake zili m’mitambo.+
115 Ife sitikuyenerera kalikonse, inu Yehova, ife sitikuyenerera kalikonse,+Koma dzina lanu ndi loyenera kulemekezedwa+Malinga ndi kukoma mtima kwanu kosatha, malinganso ndi choonadi chanu.+