Yobu 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 n’kuyamba kunena kuti:“Ndinatuluka m’mimba mwa mayi anga ndili wamaliseche,+Ndipo ndidzabwerera mmenemo ndilinso wamaliseche.+Yehova wapereka,+ ndipo Yehova yemweyo watenga.+Dzina la Yehova lipitirize kutamandidwa.”+ 1 Timoteyo 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti sitinabwere ndi kanthu m’dziko, ndipo sitingatulukemo ndi kanthu.+
21 n’kuyamba kunena kuti:“Ndinatuluka m’mimba mwa mayi anga ndili wamaliseche,+Ndipo ndidzabwerera mmenemo ndilinso wamaliseche.+Yehova wapereka,+ ndipo Yehova yemweyo watenga.+Dzina la Yehova lipitirize kutamandidwa.”+