1 Mbiri 16:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Vomerezani Yehova, inu mabanja a mitundu ya anthu,M’patseni Yehova ulemerero ndi kuvomereza kuti iye ndi wamphamvu.+ Salimo 29:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 M’patseni Yehova, inu amphamvu,*M’patseni Yehova ulemerero ndipo vomerezani kuti iye ndi wamphamvu.+ Salimo 96:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ulemu ndi ulemerero zili pamaso pake.+Mphamvu ndi kukongola zili m’nyumba yake yopatulika.+
28 Vomerezani Yehova, inu mabanja a mitundu ya anthu,M’patseni Yehova ulemerero ndi kuvomereza kuti iye ndi wamphamvu.+
29 M’patseni Yehova, inu amphamvu,*M’patseni Yehova ulemerero ndipo vomerezani kuti iye ndi wamphamvu.+