-
Salimo 104:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
104 Tamanda Yehova, iwe moyo wanga.+
Inu Yehova Mulungu wanga, mwasonyeza kuti ndinu wamkulu koposa.+
Mwadziveka ulemu ndi ulemerero.+
-
Ezekieli 1:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Ndinaona chinachake chowala ngati siliva wosakanikirana ndi golide,+ chooneka ngati kuti mkati mwake monse mukuyaka moto.+ Kuchokera pa chimene chinali kuoneka ngati chiuno chake kupita m’mwamba ndiponso kutsika m’munsi, munthuyo anali kuoneka ngati moto, ndipo pamalo onse omuzungulira panali powala.
-
-
-