Deuteronomo 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pakuti Yehova Mulungu wanu ndi moto wowononga,+ iye ndi Mulungu wofuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha basi.*+ Salimo 104:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mwadzifunditsa kuwala ngati chofunda,+Mwatambasula kumwamba ngati nsalu ya chihema.+
24 Pakuti Yehova Mulungu wanu ndi moto wowononga,+ iye ndi Mulungu wofuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha basi.*+