Salimo 148:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Onse, anthu ndi nyama, atamande dzina la Yehova,+Pakuti dzina lake lokhalo lili pamwamba posafikirika.+Ulemerero wake uli pamwamba kuposa dziko lapansi ndi kumwamba.+ Yesaya 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Aliyense anali kuuza mnzake kuti: “Woyera, woyera, woyera ndiye Yehova wa makamu.+ Zonse zimene zili padziko lapansi zimasonyeza ulemerero wake.”
13 Onse, anthu ndi nyama, atamande dzina la Yehova,+Pakuti dzina lake lokhalo lili pamwamba posafikirika.+Ulemerero wake uli pamwamba kuposa dziko lapansi ndi kumwamba.+
3 Aliyense anali kuuza mnzake kuti: “Woyera, woyera, woyera ndiye Yehova wa makamu.+ Zonse zimene zili padziko lapansi zimasonyeza ulemerero wake.”