Salimo 148:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anthu komanso zolengedwa zina zonse, atamande dzina la Yehova,Chifukwa dzina lake lokhalo lili pamwamba poti aliyense sangafikepo.+ Ulemerero wake uli pamwamba kuposa dziko lapansi ndi kumwamba.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 148:13 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 20
13 Anthu komanso zolengedwa zina zonse, atamande dzina la Yehova,Chifukwa dzina lake lokhalo lili pamwamba poti aliyense sangafikepo.+ Ulemerero wake uli pamwamba kuposa dziko lapansi ndi kumwamba.+