Salimo 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu Yehova Ambuye wathu, dzina lanu ndi lalikulu padziko lonse lapansi,+Inuyo ulemerero wanu ukusimbidwa kumwambamwamba!+ Yesaya 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 M’tsiku limenelo mudzanenadi kuti: “Yamikani Yehova anthu inu.+ Itanani pa dzina lake.+ Dziwitsani mitundu ya anthu zochita zake.+ Nenani kuti dzina lake n’lokwezeka.+
8 Inu Yehova Ambuye wathu, dzina lanu ndi lalikulu padziko lonse lapansi,+Inuyo ulemerero wanu ukusimbidwa kumwambamwamba!+
4 M’tsiku limenelo mudzanenadi kuti: “Yamikani Yehova anthu inu.+ Itanani pa dzina lake.+ Dziwitsani mitundu ya anthu zochita zake.+ Nenani kuti dzina lake n’lokwezeka.+