Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 8:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 “Koma kodi Mulungu angakhaledi padziko lapansi?+ Taonani! Kumwamba,+ ngakhale kumwambamwamba,+ simungakwaneko.+ Kuli bwanji nyumba+ imene ndamangayi?

  • 1 Mbiri 16:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Ulemu ndi ulemerero zili pamaso pake,+

      Pokhala pake pali mphamvu ndi chimwemwe.+

  • Yobu 37:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Kunyezimira ngati kwa golide kumachokera kumpoto.

      Ulemu+ wa Mulungu ndi wochititsa mantha.

  • Salimo 104:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 104 Tamanda Yehova, iwe moyo wanga.+

      Inu Yehova Mulungu wanga, mwasonyeza kuti ndinu wamkulu koposa.+

      Mwadziveka ulemu ndi ulemerero.+

  • Salimo 148:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Onse, anthu ndi nyama, atamande dzina la Yehova,+

      Pakuti dzina lake lokhalo lili pamwamba posafikirika.+

      Ulemerero wake uli pamwamba kuposa dziko lapansi ndi kumwamba.+

  • Yesaya 33:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Koma kumeneko, Yehova Wolemekezeka+ adzakhala malo a mitsinje+ ndi a ngalande zikuluzikulu kwa ife. Kumalo amenewo sikudzadutsa gulu la ngalawa kapena zombo zikuluzikulu.

  • Aheberi 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Iye amasonyeza ndendende mmene ulemerero wa Mulungu ulili+ ndipo ndiye chithunzi chenicheni cha Mulungu weniweniyo,+ ndipo amachirikiza zinthu zonse mwa mawu ake amphamvu.+ Atatiyeretsa potichotsera machimo athu,+ anakhala pansi kudzanja lamanja+ la Wolemekezeka m’malo okwezeka.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena