Salimo 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Inu Yehova Ambuye wathu, dzina lanu ndi lalikulu padziko lonse lapansi!+ Salimo 93:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ulemerero wa Yehova ndi waukulu+ kumwamba,Kuposa mkokomo wa madzi ambiri, kuposanso mafunde amphamvu a m’nyanja.+ Luka 9:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Pamenepo, onse anadabwa ndi mphamvu zodabwitsa+ za Mulungu. Tsopano onse adakali odabwa ndi zonse zimene anali kuchita, Yesu anauza ophunzira ake kuti: Aheberi 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiye kunena za zinthu zimene tikukambiranazi, mfundo yaikulu ndi iyi: Tili ndi mkulu wa ansembe+ ngati ameneyu, ndipo iye wakhala pansi kumwamba, kudzanja lamanja la mpando wachifumu wa Wolemekezeka.+
4 Ulemerero wa Yehova ndi waukulu+ kumwamba,Kuposa mkokomo wa madzi ambiri, kuposanso mafunde amphamvu a m’nyanja.+
43 Pamenepo, onse anadabwa ndi mphamvu zodabwitsa+ za Mulungu. Tsopano onse adakali odabwa ndi zonse zimene anali kuchita, Yesu anauza ophunzira ake kuti:
8 Ndiye kunena za zinthu zimene tikukambiranazi, mfundo yaikulu ndi iyi: Tili ndi mkulu wa ansembe+ ngati ameneyu, ndipo iye wakhala pansi kumwamba, kudzanja lamanja la mpando wachifumu wa Wolemekezeka.+