Deuteronomo 28:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 “Ngati sudzatsatira mosamala mawu onse a chilamulo ichi olembedwa m’buku ili,+ kuti uziopa dzina laulemerero+ ndi lochititsa manthali,+ dzina lakuti Yehova,+ amene ndi Mulungu wako, Salimo 148:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Onse, anthu ndi nyama, atamande dzina la Yehova,+Pakuti dzina lake lokhalo lili pamwamba posafikirika.+Ulemerero wake uli pamwamba kuposa dziko lapansi ndi kumwamba.+ Mateyu 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Koma inu muzipemphera motere:+ “‘Atate wathu wakumwamba, dzina+ lanu liyeretsedwe.+ Yohane 17:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ine ndachititsa kuti iwo adziwe dzina lanu+ ndipo ndidzapitiriza kuwadziwitsa dzinalo kuti chikondi chimene munandikonda nacho chikhale mwa iwo, inenso ndikhale wogwirizana ndi iwo.”+
58 “Ngati sudzatsatira mosamala mawu onse a chilamulo ichi olembedwa m’buku ili,+ kuti uziopa dzina laulemerero+ ndi lochititsa manthali,+ dzina lakuti Yehova,+ amene ndi Mulungu wako,
13 Onse, anthu ndi nyama, atamande dzina la Yehova,+Pakuti dzina lake lokhalo lili pamwamba posafikirika.+Ulemerero wake uli pamwamba kuposa dziko lapansi ndi kumwamba.+
26 Ine ndachititsa kuti iwo adziwe dzina lanu+ ndipo ndidzapitiriza kuwadziwitsa dzinalo kuti chikondi chimene munandikonda nacho chikhale mwa iwo, inenso ndikhale wogwirizana ndi iwo.”+