Ekisodo 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno anatenga buku la pangano+ ndi kuwerengera anthuwo kuti amve.+ Zitatero anthuwo anati: “Zonse zimene Yehova wanena tidzachita zomwezo ndipo tidzamumvera.”+ Levitiko 26:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 ndipo mukadzakana malangizo anga,+ n’kunyansidwa ndi zigamulo zanga, moti mwakana kutsatira malamulo anga onse, n’kufika pophwanya pangano langa,+ Deuteronomo 31:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Tengani buku ili la chilamulo,+ muliike pambali pa likasa+ la pangano la Yehova Mulungu wanu, kuti likhale mboni ya Mulungu yokutsutsani.+
7 Ndiyeno anatenga buku la pangano+ ndi kuwerengera anthuwo kuti amve.+ Zitatero anthuwo anati: “Zonse zimene Yehova wanena tidzachita zomwezo ndipo tidzamumvera.”+
15 ndipo mukadzakana malangizo anga,+ n’kunyansidwa ndi zigamulo zanga, moti mwakana kutsatira malamulo anga onse, n’kufika pophwanya pangano langa,+
26 “Tengani buku ili la chilamulo,+ muliike pambali pa likasa+ la pangano la Yehova Mulungu wanu, kuti likhale mboni ya Mulungu yokutsutsani.+