Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 14:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Pamenepo ndidzalola Farao kuumitsa mtima wake,+ ndipo adzawathamangira. Ndidzapezerapo ulemerero mwa kugonjetsa Farao ndi magulu ake onse ankhondo,+ ndipo Aiguputo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.”+ Choncho Aisiraeli anachitadi momwemo.

  • Levitiko 10:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Chotero Mose anauza Aroni kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Anthu amene ali pafupi ndi ine+ ayenera kundiona kukhala woyera,+ ndipo anthu onse azindipatsa ulemerero.’”+ Pamenepo Aroni anangokhala chete.

  • Salimo 72:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Lidalitsike dzina lake laulemerero mpaka kalekale,+

      Ndipo ulemerero wake udzaze dziko lonse lapansi.+

      Ame! Ame!*

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena