Ekisodo 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamenepo Aiguputo adzadziwa kuti ine ndine Yehova ndikadzatambasula dzanja langa ndi kukantha Iguputo.+ Motero ndidzatulutsa ana a Isiraeli m’dzikolo.”+ Ekisodo 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pa tsiku limenelo ndidzapatula dera la Goseni kumene kuli anthu anga, kuti kusakhale tizilombo toyamwa magazi.+ Ndidzatero kuti udziwe kuti ine ndine Yehova, ndipo ndili ndi mphamvu padziko lonse lapansi.+ Salimo 83:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kuti anthu adziwe+ kuti inu, amene dzina lanu ndinu Yehova,+Inu nokha ndinu Wam’mwambamwamba,+ wolamulira dziko lonse lapansi.+ Ezekieli 26:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 ‘Anthu a m’midzi yake yozungulira imene ili kunja kwa mzindawo adzaphedwa ndi lupanga, ndipo anthu adzadziwa kuti ine ndine Yehova.’+
5 Pamenepo Aiguputo adzadziwa kuti ine ndine Yehova ndikadzatambasula dzanja langa ndi kukantha Iguputo.+ Motero ndidzatulutsa ana a Isiraeli m’dzikolo.”+
22 Pa tsiku limenelo ndidzapatula dera la Goseni kumene kuli anthu anga, kuti kusakhale tizilombo toyamwa magazi.+ Ndidzatero kuti udziwe kuti ine ndine Yehova, ndipo ndili ndi mphamvu padziko lonse lapansi.+
18 Kuti anthu adziwe+ kuti inu, amene dzina lanu ndinu Yehova,+Inu nokha ndinu Wam’mwambamwamba,+ wolamulira dziko lonse lapansi.+
6 ‘Anthu a m’midzi yake yozungulira imene ili kunja kwa mzindawo adzaphedwa ndi lupanga, ndipo anthu adzadziwa kuti ine ndine Yehova.’+