Deuteronomo 32:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti ndidzalengeza dzina la Yehova.+Vomerezani ukulu wa Mulungu wathu!+ Mateyu 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Koma inu muzipemphera motere:+ “‘Atate wathu wakumwamba, dzina+ lanu liyeretsedwe.+ Yohane 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Anthu amene munawatenga m’dziko ndi kundipatsa ine ndawadziwitsa dzina lanu.+ Anali anu, koma munawapereka kwa ine, ndipo iwo asunga mawu anu.
6 “Anthu amene munawatenga m’dziko ndi kundipatsa ine ndawadziwitsa dzina lanu.+ Anali anu, koma munawapereka kwa ine, ndipo iwo asunga mawu anu.