Ekisodo 34:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamenepo Yehova anatsika+ mumtambo ndi kuimirira pafupi ndi Mose, n’kulengeza dzina lake lakuti Yehova.+ Salimo 105:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 105 YAMIKANI Yehova, itanani pa dzina lake,+Lengezani zochita zake pakati pa mitundu ya anthu.+ Yohane 17:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ine ndachititsa kuti iwo adziwe dzina lanu+ ndipo ndidzapitiriza kuwadziwitsa dzinalo kuti chikondi chimene munandikonda nacho chikhale mwa iwo, inenso ndikhale wogwirizana ndi iwo.”+
5 Pamenepo Yehova anatsika+ mumtambo ndi kuimirira pafupi ndi Mose, n’kulengeza dzina lake lakuti Yehova.+
26 Ine ndachititsa kuti iwo adziwe dzina lanu+ ndipo ndidzapitiriza kuwadziwitsa dzinalo kuti chikondi chimene munandikonda nacho chikhale mwa iwo, inenso ndikhale wogwirizana ndi iwo.”+