Ekisodo 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndinali kuonekera kwa Abulahamu,+ Isaki+ ndi Yakobo+ monga Mulungu Wamphamvuyonse.+ Koma za dzina langa lakuti Yehova,+ ine sindinadzidziwikitse+ kwa iwo. Ekisodo 33:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma Mulungu anati: “Ineyo ndidzakuonetsa ubwino wanga wonse,+ ndipo ndidzalengeza dzina langa lakuti Yehova kwa iwe.+ Amene ndikufuna kum’komera mtima ndidzam’komera mtima, ndipo amene ndikufuna kum’sonyeza chifundo, ndidzam’sonyeza chifundo.”+
3 Ndinali kuonekera kwa Abulahamu,+ Isaki+ ndi Yakobo+ monga Mulungu Wamphamvuyonse.+ Koma za dzina langa lakuti Yehova,+ ine sindinadzidziwikitse+ kwa iwo.
19 Koma Mulungu anati: “Ineyo ndidzakuonetsa ubwino wanga wonse,+ ndipo ndidzalengeza dzina langa lakuti Yehova kwa iwe.+ Amene ndikufuna kum’komera mtima ndidzam’komera mtima, ndipo amene ndikufuna kum’sonyeza chifundo, ndidzam’sonyeza chifundo.”+