Salimo 89:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 89 Ndidzaimba mpaka kalekale za ntchito za Yehova zosonyeza kukoma mtima kwake kosatha.+Ndidzalengeza ndi pakamwa panga ku mibadwomibadwo za kukhulupirika kwanu.+ Salimo 96:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Lengezani ulemerero wake pakati pa anthu a mitundu ina,+Ndiponso ntchito zake zodabwitsa pakati pa mitundu yonse ya anthu.+ Salimo 145:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kuti ana a anthu adziwe za ntchito zanu zamphamvu+Ndi kukula kwa ulemerero wa ufumu wanu.+
89 Ndidzaimba mpaka kalekale za ntchito za Yehova zosonyeza kukoma mtima kwake kosatha.+Ndidzalengeza ndi pakamwa panga ku mibadwomibadwo za kukhulupirika kwanu.+
3 Lengezani ulemerero wake pakati pa anthu a mitundu ina,+Ndiponso ntchito zake zodabwitsa pakati pa mitundu yonse ya anthu.+