Salimo 98:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 98 IMBIRANI Yehova nyimbo yatsopano,+Pakuti zimene wachita ndi zodabwitsa.+Dzanja lake lamanja, ndithu mkono wake woyera, wabweretsa chipulumutso.+ Salimo 136:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yamikani Wochita zodabwitsa ndiponso ntchito zazikulu:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+
98 IMBIRANI Yehova nyimbo yatsopano,+Pakuti zimene wachita ndi zodabwitsa.+Dzanja lake lamanja, ndithu mkono wake woyera, wabweretsa chipulumutso.+
4 Yamikani Wochita zodabwitsa ndiponso ntchito zazikulu:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+