Salimo 22:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndidzalengeza dzina lanu+ kwa abale anga.+Ndidzakutamandani pakati pa mpingo.+ Yohane 10:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Chimene Atate+ wanga wandipatsa n’chofunika kuposa zinthu zonse,+ ndipo palibe amene angazitsomphole m’dzanja la Atate.+ Machitidwe 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Sumeoni+ wafotokoza bwino mmene Mulungu anacheukira anthu a mitundu ina kwa nthawi yoyamba, kuti mwa iwo atengemo anthu odziwika ndi dzina lake.+ Aheberi 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 pamene akunena kuti: “Ndidzalengeza dzina lanu kwa abale anga. Ndidzakutamandani mwa kuimba nyimbo pakati pa mpingo.”+
29 Chimene Atate+ wanga wandipatsa n’chofunika kuposa zinthu zonse,+ ndipo palibe amene angazitsomphole m’dzanja la Atate.+
14 Sumeoni+ wafotokoza bwino mmene Mulungu anacheukira anthu a mitundu ina kwa nthawi yoyamba, kuti mwa iwo atengemo anthu odziwika ndi dzina lake.+
12 pamene akunena kuti: “Ndidzalengeza dzina lanu kwa abale anga. Ndidzakutamandani mwa kuimba nyimbo pakati pa mpingo.”+