Salimo 22:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndidzalengeza dzina lanu+ kwa abale anga.+Ndidzakutamandani pakati pa mpingo.+ Salimo 40:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndanena za uthenga wabwino wachilungamo mumpingo waukulu.+Onani! Sindinatseke pakamwa panga.+Inu Yehova, mukudziwa bwino zimenezi.+ Luka 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno anayamba kuwauza kuti: “Lero lemba ili, limene mwangolimva kumeneli lakwaniritsidwa.”+ Luka 19:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Iye anati: “Iwe ukanazindikira+ lero zinthu zamtendere . . . koma tsopano zabisika kuti usathe kuziona.+
9 Ndanena za uthenga wabwino wachilungamo mumpingo waukulu.+Onani! Sindinatseke pakamwa panga.+Inu Yehova, mukudziwa bwino zimenezi.+
42 Iye anati: “Iwe ukanazindikira+ lero zinthu zamtendere . . . koma tsopano zabisika kuti usathe kuziona.+