Mateyu 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Musaganize kuti ndinabwera kudzawononga Chilamulo+ kapena Zolemba za aneneri. Sindinabwere kudzaziwononga koma kudzazikwaniritsa.+ 2 Akorinto 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti iye anati: “Pa nthawi yovomerezedwa ndinakumvera, ndipo m’tsiku lachipulumutso ndinakuthandiza.”+ Ndithudi, inoyo ndiyo nthawi yeniyeni yovomerezedwa.+ Linolo ndilo tsiku lachipulumutso.+
17 “Musaganize kuti ndinabwera kudzawononga Chilamulo+ kapena Zolemba za aneneri. Sindinabwere kudzaziwononga koma kudzazikwaniritsa.+
2 Pakuti iye anati: “Pa nthawi yovomerezedwa ndinakumvera, ndipo m’tsiku lachipulumutso ndinakuthandiza.”+ Ndithudi, inoyo ndiyo nthawi yeniyeni yovomerezedwa.+ Linolo ndilo tsiku lachipulumutso.+