Yohane 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tiyenera kugwira ntchito za iye amene anandituma ine kudakali masana.+ Usiku+ ukubwera pamene munthu sangathe kugwira ntchito. Aheberi 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 M’malomwake, pitirizani kudandaulirana+ tsiku ndi tsiku, nthawi iliyonse imene mukuti “Lero,”+ kuopera kuti chinyengo+ champhamvu cha uchimo chingaumitse mtima wa wina wa inu.
4 Tiyenera kugwira ntchito za iye amene anandituma ine kudakali masana.+ Usiku+ ukubwera pamene munthu sangathe kugwira ntchito.
13 M’malomwake, pitirizani kudandaulirana+ tsiku ndi tsiku, nthawi iliyonse imene mukuti “Lero,”+ kuopera kuti chinyengo+ champhamvu cha uchimo chingaumitse mtima wa wina wa inu.