Maliko 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 koma nkhawa+ za m’nthawi* ino, chinyengo champhamvu cha chuma,+ komanso zilakolako+ za zinthu zina, zimalowa ndi kulepheretsa mawuwo kukula, ndipo sabala zipatso.+ 2 Atesalonika 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ndi kusalungama ndi chinyengo chilichonse.+ Zonsezi adzazichita kwa amene akupita kukawonongedwa.+ Izi zidzakhala chilango kwa iwo chifukwa sanasonyeze kuti akulakalaka+ choonadi, kuti apulumuke.+
19 koma nkhawa+ za m’nthawi* ino, chinyengo champhamvu cha chuma,+ komanso zilakolako+ za zinthu zina, zimalowa ndi kulepheretsa mawuwo kukula, ndipo sabala zipatso.+
10 ndi kusalungama ndi chinyengo chilichonse.+ Zonsezi adzazichita kwa amene akupita kukawonongedwa.+ Izi zidzakhala chilango kwa iwo chifukwa sanasonyeze kuti akulakalaka+ choonadi, kuti apulumuke.+