Mateyu 24:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kudzafika aneneri ambiri onyenga+ ndipo adzasocheretsa anthu ambiri.+ 2 Akorinto 11:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti amuna oterowo ndi atumwi onama, antchito achinyengo,+ odzisandutsa atumwi a Khristu.+