Mateyu 24:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chifukwa cha kuwonjezeka kwa kusamvera malamulo,+ chikondi cha anthu ambiri chidzazirala.+ Yuda 19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Anthu amenewa ndiwo amayambitsa magawano,+ amachita zauchinyama,+ ndipo alibe mzimu wa Mulungu.+