Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Luka 11:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Amene sali kumbali yanga akutsutsana ndi ine, ndipo amene sasonkhanitsa anthu pamodzi ndi ine amawabalalitsa.+

  • Aroma 16:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Tsopano ndikukudandaulirani abale, kuti musamale ndi anthu amene amayambitsa magawano+ ndi kuchita zinthu zokhumudwitsa ena. Zimenezi ndi zosemphana ndi chiphunzitso+ chimene munaphunzira, choncho muziwapewa.+

  • 1 Akorinto 1:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Tsopano ndikukudandaulirani+ abale, m’dzina+ la Ambuye wathu Yesu Khristu, kuti nonse muzilankhula mogwirizana ndi kuti pasakhale magawano+ pakati panu, koma kuti mukhale ogwirizana+ pokhala ndi mtima umodzi ndi maganizo amodzi.+

  • Yakobo 3:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Pakuti pamene pali nsanje+ ndi mtima wokonda mikangano, palinso chisokonezo ndi zoipa zamtundu uliwonse.+

  • 3 Yohane 10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 N’chifukwa chake ndikadzabwera, ndidzaulula ntchito zake zimene akupitirizabe kuchita.+ Iye amatinenera zamwano,+ komanso chifukwa chosakhutira ndi zinthu zimenezi, iye salandira abalewo+ mwaulemu, ndipo amene amafuna kulandira+ abalewo, amawatsekereza+ ndi kuwachotsa+ mumpingo.

  • Chivumbulutso 2:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ndiponso uli ndi olimbikira chiphunzitso cha mpatuko wa Nikolao.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena