Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 23:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Kodi maso ako amayang’anitsitsa chuma, pomwe icho sichichedwa kuchoka?+ Chifukwa ndithu chimadzipangira mapiko ngati a chiwombankhanga n’kuulukira kumwamba.+

  • Maliko 10:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Yesu anayang’ana uku ndi uku, kenako anauza ophunzira akewo kuti: “Zidzakhalatu zovuta kwambiri kuti anthu andalama+ adzalowe mu ufumu wa Mulungu!”+

  • Luka 18:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Yesu anamuyang’ana n’kunena kuti: “Zidzakhalatu zovuta kwambiri kuti anthu a ndalama adzalowe mu ufumu wa Mulungu!+

  • 1 Timoteyo 6:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Komabe, anthu ofunitsitsa kulemera, amagwera m’mayesero+ ndi mumsampha. Iwo amakodwa ndi zilakolako zambiri zowapweteketsa ndiponso amachita zinthu mopanda nzeru.+ Zinthu zimenezi zimawawononga ndi kuwabweretsera mavuto.+

  • 2 Timoteyo 4:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pakuti Dema+ wandisiya chifukwa chokonda zinthu za m’nthawi* ino,+ ndipo wapita ku Tesalonika. Keresike wapita ku Galatiya,+ ndipo Tito wapita ku Dalimatiya.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena