Miyambo 28:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Munthu wochita zinthu mokhulupirika adzapeza madalitso ambiri,+ koma woyesetsa kuti apeze chuma mofulumira, sadzapitiriza kukhala wosalakwa.+ Miyambo 28:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Munthu wanjiru amayesetsa kuti apeze zinthu zamtengo wapatali,+ koma sadziwa kuti umphawi udzamugwera.
20 Munthu wochita zinthu mokhulupirika adzapeza madalitso ambiri,+ koma woyesetsa kuti apeze chuma mofulumira, sadzapitiriza kukhala wosalakwa.+
22 Munthu wanjiru amayesetsa kuti apeze zinthu zamtengo wapatali,+ koma sadziwa kuti umphawi udzamugwera.