1 Samueli 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho Davide anayamba kupita kunkhondo. Kulikonse kumene Sauli wamutumiza anali kuchita zinthu mwanzeru,+ moti Sauli anamuika kukhala woyang’anira asilikali.+ Zimenezi zinasangalatsa anthu onse komanso atumiki a Sauli. Nehemiya 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Zitatero ndinaika Haneni+ m’bale wanga ndi Hananiya kalonga wa m’Nyumba ya Chitetezo Champhamvu,+ kuti aziyang’anira Yerusalemu. Hananiya anali munthu wodalirika+ ndipo anali woopa kwambiri+ Mulungu woona kuposa anthu ena ambiri. Salimo 101:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Maso anga ali pa okhulupirika a padziko lapansi,+Kuti akhale ndi ine.+Woyenda m’njira yowongoka,+Ndi amene adzanditumikira.+
5 Choncho Davide anayamba kupita kunkhondo. Kulikonse kumene Sauli wamutumiza anali kuchita zinthu mwanzeru,+ moti Sauli anamuika kukhala woyang’anira asilikali.+ Zimenezi zinasangalatsa anthu onse komanso atumiki a Sauli.
2 Zitatero ndinaika Haneni+ m’bale wanga ndi Hananiya kalonga wa m’Nyumba ya Chitetezo Champhamvu,+ kuti aziyang’anira Yerusalemu. Hananiya anali munthu wodalirika+ ndipo anali woopa kwambiri+ Mulungu woona kuposa anthu ena ambiri.
6 Maso anga ali pa okhulupirika a padziko lapansi,+Kuti akhale ndi ine.+Woyenda m’njira yowongoka,+Ndi amene adzanditumikira.+