2 Akorinto 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pomalizira abale, ndikuti pitirizani kukondwera, kusintha maganizo anu, kulimbikitsidwa,+ kukhala ndi maganizo ogwirizana,+ ndiponso kukhala mwamtendere.+ Mukatero, Mulungu wachikondi ndi wamtendere+ adzakhala nanu.
11 Pomalizira abale, ndikuti pitirizani kukondwera, kusintha maganizo anu, kulimbikitsidwa,+ kukhala ndi maganizo ogwirizana,+ ndiponso kukhala mwamtendere.+ Mukatero, Mulungu wachikondi ndi wamtendere+ adzakhala nanu.