Salimo 101:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Maso anga ali pa okhulupirika a padziko lapansi,+Kuti akhale ndi ine.+Woyenda m’njira yowongoka,+Ndi amene adzanditumikira.+ Miyambo 28:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Munthu wochita zinthu mokhulupirika adzapeza madalitso ambiri,+ koma woyesetsa kuti apeze chuma mofulumira, sadzapitiriza kukhala wosalakwa.+ Machitidwe 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chotero abale, fufuzani+ pakati panu amuna 7 a mbiri yabwino, amene ali ndi mzimu komanso nzeru zochuluka,+ kuti ife tiwaike kukhala oyang’anira ntchito yofunikayi. 1 Akorinto 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Komanso pamenepa, chofunika kwa woyang’anira+ ndicho kukhala wokhulupirika.+
6 Maso anga ali pa okhulupirika a padziko lapansi,+Kuti akhale ndi ine.+Woyenda m’njira yowongoka,+Ndi amene adzanditumikira.+
20 Munthu wochita zinthu mokhulupirika adzapeza madalitso ambiri,+ koma woyesetsa kuti apeze chuma mofulumira, sadzapitiriza kukhala wosalakwa.+
3 Chotero abale, fufuzani+ pakati panu amuna 7 a mbiri yabwino, amene ali ndi mzimu komanso nzeru zochuluka,+ kuti ife tiwaike kukhala oyang’anira ntchito yofunikayi.