Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 5:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Gehazi anayankha kuti: “Inde n’kwabwino. Mbuyanga+ wandituma+ kuti, ‘Posachedwapa kwabwera anyamata awiri, ana a aneneri,+ kuchokera kudera lamapiri la Efuraimu. Muwapatseko talente imodzi ya siliva ndi zovala ziwiri.’”+

  • Miyambo 20:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Cholowa chopezedwa mwadyera poyamba,+ tsogolo lake silidzadalitsidwa.+

  • Yeremiya 17:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Munthu wopeza chuma mopanda chilungamo+ ali ngati nkhwali imene yasonkhanitsa mazira amene sinaikire. Chuma chakecho adzachisiya asanakwanitse ngakhale hafu ya zaka za moyo wake,+ ndipo pamapeto pake adzaonekera kuti ndi wopusa.”+

  • 1 Timoteyo 6:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Komabe, anthu ofunitsitsa kulemera, amagwera m’mayesero+ ndi mumsampha. Iwo amakodwa ndi zilakolako zambiri zowapweteketsa ndiponso amachita zinthu mopanda nzeru.+ Zinthu zimenezi zimawawononga ndi kuwabweretsera mavuto.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena