Mateyu 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Zimene zafesedwa paminga, ndi munthu amene amamva mawu, koma nkhawa za moyo wa m’nthawi* ino+ ndiponso chinyengo champhamvu cha chuma zimalepheretsa mawuwo kukula, ndipo iye amakhala wosabala zipatso.+ Yakobo 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tamverani tsopano inu anthu achuma.+ Lirani, fuulani chifukwa cha masautso amene akubwera kwa inu.+
22 Zimene zafesedwa paminga, ndi munthu amene amamva mawu, koma nkhawa za moyo wa m’nthawi* ino+ ndiponso chinyengo champhamvu cha chuma zimalepheretsa mawuwo kukula, ndipo iye amakhala wosabala zipatso.+
5 Tamverani tsopano inu anthu achuma.+ Lirani, fuulani chifukwa cha masautso amene akubwera kwa inu.+