Luka 12:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako anauza ophunzira ake kuti: “Pa chifukwa chimenechi ndikukuuzani kuti, Lekani kudera nkhawa moyo wanu kuti mudzadya chiyani kapena kudera nkhawa matupi anu kuti mudzavala chiyani.+
22 Kenako anauza ophunzira ake kuti: “Pa chifukwa chimenechi ndikukuuzani kuti, Lekani kudera nkhawa moyo wanu kuti mudzadya chiyani kapena kudera nkhawa matupi anu kuti mudzavala chiyani.+