Miyambo 11:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Wodalira chuma chake adzagwa,+ koma anthu olungama adzasangalala ngati masamba a zomera.+